Kwabwera Edzi nthenda yoopsa = There is AIDS, a killer disease

Title

Kwabwera Edzi nthenda yoopsa = There is AIDS, a killer disease

Date

2004-06-08

Language

Type

Identifier

MD 3.3

Coverage

Rumphi District

Transcription

Kwabwera Edzi nthenda yoopsa/nthenda yopanda mankhwala iyi
There is AIDS, a killer disease/the disease which has no cure
Tayendayenda maiko oase/osawapeza mankhwala a Edzi
I searched the whole world for the drug/but I cannot find any cure for AIDS

Tikulira oh ndi nthenda iyi/Usalire oh mphavu zinaliko
We are crying because of the disease/Don’t cry, we can fight the disease

Apita mai ndi nthenda iyi/apita bambo ndi nthenda iyi
My mom has died of the disease/my dad has died of the disease
Ndasala ndekha ndikulira ndizatani makolo apita
I’m just alone crying, and what am I going to do? My parents have gone

Ndaphunzira oh za nthenda iyi/Ndaphunzira oh kupewa Edzi
I have learned of this disease/I have learned to prevent AIDS

[Spoken]
Usalire mwana wanga, maphunziro ndiye tsogolo lako ukasunga khosi nkanda woyela udzavala
Don’t cry my child, education is your future
Taphunzira za matenda a Edzi/katengedwe kake kafalitsidwe kake ndi kapewedwe kake
We learned of the disease AIDS/how you can get it, how it is spread, how it is prevented

Tikulira oh ndi nthenda iyi/Usalire oh mphavu zinaliko
We are crying because of the disease/Don’t cry, we can fight the disease