Oh azanga, ndifuna ndifunse = Oh my friends, I want to ask [take 2]

Title

Oh azanga, ndifuna ndifunse = Oh my friends, I want to ask [take 2]

Date

2004-06-22

Language

Type

Identifier

MD 7.18

Coverage

Rumphi District

Transcription

Oh azanga, ndifuna ndifunse/Ndamva kuti Edzi/Edzi ndi chiyani?
Oh my friends, I want to ask/I heard of AIDS/What is AIDS?
Edzi ndi matenda omwe agwedeza dziko
AIDS is a disease which has shaken the world
Zambia agwedeza dziko/Malawi agwedeza dziko/Tanzania agwedeza dziko
Zambia is shaken by it/Malawi is shaken by it/Tanzania is shaken by it
Azibambo ambiri anamwali ndi matendawa/Azimayi ambiri anamwali ndi matendawa
More fathers have died of the disease/More mothers have died of the disease
Anyamata ndi asungwana bwerani tikambirane kugonjetsa nthendayi
Boys and girls, let’s discuss how to conquer the disease
Ndikulimbika maphunziro/Ana amasiye achuluka/Makolo awo anamwali ndi matendawa
Work hard on education/The number of orphans is going up/Their parents died of the disease